Lyrics Timed, click a line to jump
(Slay) you already know
She said, "Kodi I'm never enough
Or you're just not in love?"
Then I said, "You're the love of my life
I can't imagine living life without you
You brighten out my days
So I can't imagine living life without you
My success means nothing without you"
Then she said, "Nanga bwanji sumasintha khalidwe?"
Ambuye (plus one)
Nzamutenge (plus one)
Ndikupempha ngati kukhale kotheka mzandipatseko plus one
Ambuye (plus one)
Nzamutenge (plus one)
Ndikupempha ngati kukhale kotheka mzandipatseko plus one
Mkaziyu ndamuzunza
Malo mowina amangoluza
Pena zimandikhudza
Ten times I've cheated on her, ah
She priceless but she's royal, royal
Carefull how you play your cards when you have a queen in your hand
Ambuye (plus one)
Nzamutenge (plus one)
Ndikupempha ngati kukhale kotheka mzandipatseko plus one
Ambuye (plus one)
Nzamutenge (plus one)
Ndikupempha ngati kukhale kotheka mzandipatseko plus one
Ndimapempha muzamutenge uyuyu
Chomwe ndamdziwitsa kwambiri ndi ululu
Sinampatse mtendere olo ufulu
Koma chomwe ndikupempha
Adzalowe nawo mu ufumu
And I'm asking ngati muzanditenge
Mudzandipatse plus one, musadzamusiye uyu chonde
Ambuye mudzamutenge uyuyu
Ndikupempha, ndikupempha ine
Ambuye mudzamutenge uyuyu
Ndikupempha, ndikupempha ineyo